![](https://malawi24.com/wp-content/uploads/2025/02/Mary-Navitcha.jpg)
A Malawi atopa ndi mavuto akufuna kusintha komwe kukubwera ndi APM pa 16 September – Navicha
Advertisement Wamkulu wa amayi kuchipani cha DPP, mayi Mary Thom Navicha wati anthu m’dziko muno atopa ndi mavuto omwe boma lilipo panoli lawayika, ndipo ali pa moto chifukwa MCP ikukanika kupeza njira zothetsela mavuto omwe akuta dziko lino. A Navicha …